Masalimo 69:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo chidzakomera Yehova koposa ng'ombe, inde mphongo za nyanga ndi ziboda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo chidzakomera Yehova koposa ng'ombe, inde mphongo za nyanga ndi ziboda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Zimenezi zidzakondwetsa Chauta kupambana nsembe, ngakhale nsembe ya ng'ombe yamphongo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Izi zidzakondweretsa Yehova kupambana ngʼombe, kupambananso ngʼombe yayimuna, pamodzi ndi nyanga ndi ziboda zake. Onani mutuwo |