Masalimo 69:30 - Buku Lopatulika30 Ndidzalemekeza dzina la Mulungu ndi kuliimbira, ndipo ndidzambukitsa ndi kumyamika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndidzalemekeza dzina la Mulungu ndi kuliimbira, ndipo ndidzambukitsa ndi kumyamika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Ndidzatamanda dzina la Mulungu pomuimbira nyimbo, ndidzalalika ukulu wake pomuthokoza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ine ndidzatamanda dzina la Mulungu mʼnyimbo, ndidzalemekeza Iye ndi chiyamiko. Onani mutuwo |