Masalimo 69:26 - Buku Lopatulika26 Pakuti alondola amene Inu munampanda; ndipo akambirana za zowawa zao za iwo amene munawalasa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Pakuti alondola amene Inu munampanda; ndipo akambirana za zowawa zao za iwo amene munawalasa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Iwo amazunza amene Inu mwamkantha, ndipo amene Inu mwamupweteka, iwo amaonjezera kumuvutitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Pakuti iwo amazunza amene inu munamuvulaza ndi kuyankhula zowawa kwa amene munawapweteka. Onani mutuwo |