Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 69:25 - Buku Lopatulika

25 Pokhala pao pakhale bwinja; m'mahema mwao musakhale munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Pokhala pao pakhale bwinja; m'mahema mwao musakhale munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Zithando zao zisanduke zopanda anthu, m'mahema mwao musatsale munthu ndi mmodzi yemwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Malo awo akhale wopanda anthu pasapezeke ndi mmodzi yemwe wokhala mʼmatenti awo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 69:25
8 Mawu Ofanana  

Ndipo munthu yense wopitirira pa nyumba yaitali ino adzadabwa nayo, nadzainyoza, nadzati, Yehova watero chifukwa ninji ndi dziko lino ndi nyumba ino?


Ndiimbire wokondedwa wanga nyimbo ya wokondedwa wanga ya munda wake wampesa. Wokondedwa wanga anali ndi munda wampesa m'chitunda cha zipatso zambiri;


Pompo ndinati ine, Ambuye mpaka liti? Ndipo anayankha, Mpaka mizinda ikhala bwinja, yopanda wokhalamo, ndi nyumba zopanda munthu, ndi dziko likhala bwinja ndithu,


Onani, nyumba yanu yasiyidwa kwa inu yabwinja.


Onani nyumba yanu isiyidwa kwa inu yabwinja; ndipo ndinena kwa inu kuti, Simudzandiona Ine, kufikira mudzati, Wolemekezeka Iye amene akudza m'dzina la Ambuye.


Pakuti kwalembedwa m'buku la Masalimo, Pogonera pake pakhale bwinja, ndipo pasakhale munthu wogonapo; ndipo uyang'aniro wake autenge wina.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa