Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 69:23 - Buku Lopatulika

23 M'maso mwao mude, kuti asapenye; ndipo munjenjemeretse m'chuuno mwao kosalekeza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 M'maso mwao mude, kuti asapenye; ndipo munjenjemeretse m'chuuno mwao kosalekeza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Maso ao achite chidima kuti asathe kupenya, ziwuno zao zizinjenjemera kosalekeza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Maso awo adetsedwe kotero kuti asaonenso ndipo misana yawo ipindike mpaka kalekale.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 69:23
12 Mawu Ofanana  

Funsani tsopano, ndi kuona ngati mwamuna aona mwana; chifukwa chanji ndiona mwamuna ndi manja ake pa chuuno chake, monga mkazi alinkubala, ndi nkhope zao zotumbuluka?


Pamenepo padasandulika pa nkhope pake pa mfumu, ndi maganizo ake anamsautsa, ndi mfundo za m'chuuno mwake zinaguluka, ndi maondo ake anaombana.


maso ao adetsedwe, kuti asapenye, ndipo muweramitse msana wao masiku onse.


Pakuti sindifuna, abale, kuti mukhale osadziwa chinsinsi ichi, kuti mungadziyese anzeru mwa inu nokha, kuti kuuma mtima kunadza pang'ono pa Israele, kufikira kudzaza kwa anthu amitundu kunalowa;


koma mitima yao inaumitsidwa; pakuti kufikira lero lomwe lino, pa kuwerenga kwa pangano lakale chophimba chomwechi chikhalabe chosavundukuka, chimene chilikuchotsedwa mwa Khristu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa