Masalimo 69:22 - Buku Lopatulika22 Gome lao likhale msampha pamaso pao; pokhala ndi mtendere iwo, likhale khwekhwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Gome lao likhale msampha pamaso pao; pokhala ndi mtendere iwo, likhale khwekhwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Zakudya zao zisanduke msampha. Akodwe ndi maphwando a nsembe zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Chakudya chomwe chayikidwa patsogolo pawo chikhale msampha; chikhale chobwezera chilango ndiponso khwekhwe. Onani mutuwo |