Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 69:2 - Buku Lopatulika

2 Ndamira m'thope lozama, lopanda poponderapo; ndalowa m'madzi ozama, ndipo chigumula chandimiza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndamira m'thope lozama, lopanda poponderapo; ndalowa m'madzi ozama, ndipo chigumula chandimiza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Ndamira m'thope lozama m'mene mulibe popondapo polimba. Ndaloŵa m'madzi ozama, ndipo mafunde andimiza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ine ndikumira mʼthope lozama mʼmene mulibe popondapo. Ndalowa mʼmadzi ozama; mafunde andimiza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 69:2
11 Mawu Ofanana  

kapena mdima kuti ungaone, ndi madzi aunyinji akumiza.


Chifukwa chake oyera mtima onse apemphere kwa Inu, pa nthawi ya kupeza Inu; indetu pakusefuka madzi aakulu sadzamfikira iye.


Ndipo anandikweza kunditulutsa m'dzenje la chitayiko, ndi m'thope la pachithaphwi; nandipondetsa pathanthwe, nakhazika mayendedwe anga.


Taonani, akazi onse otsala m'nyumba ya mfumu ya Yuda adzatulutsidwa kunka kwa akulu a mfumu ya ku Babiloni, ndipo akaziwo adzati, Oyanjana nanu anakunyengani, ndi kukuposani inu, mapazi anu amire m'thope, abwerera m'mbuyo.


Ndipo anatenga Yeremiya, namponya iye m'dzenje la Malikiya mwana wake wa mfumu, limene linali m'bwalo la kaidi; ndipo anamtsitsa Yeremiya ndi zingwe. Koma m'dzenjemo munalibe madzi, koma thope; namira Yeremiya m'thopemo.


Ndinatsikira kumatsinde a mapiri, mipingiridzo ya dziko inanditsekereza kosatha; koma munandikwezera moyo wanga kuuchotsa kuchionongeko, Yehova Mulungu wanga.


ndipo inagwa mvula, nidzala mitsinje, ndipo zinaomba mphepo, zinagunda pa nyumbayo; koma siinagwe; chifukwa inakhazikika pathanthwepo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa