Masalimo 69:1 - Buku Lopatulika1 Ndipulumutseni Mulungu; pakuti madzi afikira moyo wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipulumutseni Mulungu; pakuti madzi afikira moyo wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu, pulumutseni, pakuti madzi ayesa m'khosi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Pulumutseni Inu Mulungu, pakuti madzi afika mʼkhosi Onani mutuwo |