Masalimo 69:16 - Buku Lopatulika16 Mundiyankhe Yehova; pakuti chifundo chanu nchokoma; munditembenukire monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Mundiyankhe Yehova; pakuti chifundo chanu nchokoma; munditembenukire monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Mundiyankhe, Inu Chauta, pakuti chikondi chanu chosasinthika nchabwino. Munditchere khutu chifukwa cha chifundo chanu chachikulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndiyankheni Inu Yehova mwa ubwino wanu wa chikondi chanu; mwa chifundo chanu chachikulu tembenukirani kwa ine. Onani mutuwo |