Masalimo 69:15 - Buku Lopatulika15 Chigumula chisandifotsere, ndipo chakuya chisandimize; ndipo asanditsekere pakamwa pake pa dzenje. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Chigumula chisandifotsere, ndipo chakuya chisandimize; ndipo asanditsekere pakamwa pake pa dzenje. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Musalole kuti chigumula chindikokolole, kapena kuti nyanja yakuya indimize. Musalole kuti manda atseke kukamwa atandimeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Musalole kuti chigumula chindimeze, kuya kusandimeze ndipo dzenje lisatseke pakamwa pake kundimiza. Onani mutuwo |