Masalimo 69:14 - Buku Lopatulika14 Mundilanditse kuthope, ndisamiremo, ndilanditseni kwa iwo akundida, ndi kwa madzi ozama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Mundilanditse kuthope, ndisamiremo, ndilanditseni kwa iwo akundida, ndi kwa madzi ozama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pulumutseni kuti ndisamire m'matope, landitseni kwa adani anga ndi ku madzi ozama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mundilanditse kuchoka mʼmatope, musalole kuti ndimire, pulumutseni ine kwa iwo amene amadana nane, kuchoka mʼmadzi ozama. Onani mutuwo |