Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 68:7 - Buku Lopatulika

7 Pakutuluka paja, Inu Mulungu, ndi kutsogolera anthu anu, pakuyenda paja Inu m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Pakutuluka paja, Inu Mulungu, ndi kutsogolera anthu anu, pakuyenda paja Inu m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Inu Mulungu, pamene munkatsogolera anthu anu, pamene munkayenda m'chipululu muja,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Pamene munatuluka kutsogolera anthu anu, Inu Mulungu, pamene munayenda kudutsa chipululu,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 68:7
10 Mawu Ofanana  

Dziko la zipatso, likhale lakhulo, chifukwa cha choipa cha iwo okhalamo.


ndiye wakuchitira chiweruzo osautsika; ndiye wakupatsa anjala chakudya; Yehova amasula akaidi.


Ndipo Yehova anawatsogolera usana ndi mtambo njo kuwatsogolera m'njira; ndi usiku ndi moto njo, wakuwawalitsira; kuti ayende usana ndi usiku;


Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wanditumiza ndikamange osweka mtima, ndikalalikire kwa am'nsinga mamasulidwe, ndi kwa omangidwa kutsegulidwa kwa m'ndende;


Wothyola wakwera pamaso pao; iwo anathyola, napita kuchipata, natuluka pomwepo; ndi mfumu yao yapita pamaso pao, ndipo Yehova awatsogolera.


Kapena kodi anayesa Mulungu kumuka ndi kudzitengera mtundu mwa mtundu wina wa anthu, ndi mayesero, ndi zizindikiro, ndi zozizwa, ndi nkhondo, ndi mwa dzanja lamphamvu, ndi mkono wotambasuka, ndi mwa zoopsa zazikulu, monga mwa zonse Yehova Mulungu wanu anakuchitirani mu Ejipito pamaso panu?


Ndipo Debora anati kwa Baraki, Nyamuka; pakuti ili ndi tsikuli Yehova wapereka Sisera m'dzanja lako; sanatuluke kodi Yehova pamaso pako? Potero Baraki anatsika kuphiri la Tabori ndi amuna zikwi khumi akumtsata.


Yehova, muja mudatuluka mu Seiri, muja mudayenda kuchokera ku thengo la Edomu, dziko linanjenjemera, thambo lomwe linakha, inde mitambo inakha madzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa