Masalimo 66:8 - Buku Lopatulika8 Lemekezani Mulungu wathu, mitundu ya anthu inu, ndipo mumveketse liu la chilemekezo chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Lemekezani Mulungu wathu, mitundu ya anthu inu, ndipo mumveketse liu la chilemekezo chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Lemekezani Mulungu wathu, inu mitundu ya anthunu, mau omtamanda Iye amveke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tamandani Mulungu wathu, inu mitundu ya anthu, mulole kuti mawu a matamando ake amveke; Onani mutuwo |
mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, chifundo chake nchosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.