Masalimo 66:6 - Buku Lopatulika6 Anasanduliza nyanja ikhale mtunda. Anaoloka mtsinje choponda pansi, apo tinakondwera mwa Iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Anasanduliza nyanja ikhale mtunda. Anaoloka mtsinje choponda pansi, apo tinakondwera mwa Iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adasandutsa nyanja kuti ikhale nthaka youma. Anthu adaoloka mtsinje uja poyenda pansi. Nchifukwa chake timukondwerere Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iye anasandutsa nyanja kukhala malo owuma, iwo anawoloka pa madzi ndi mapazi. Bwerani, tiyeni tikondwere mwa Iye. Onani mutuwo |