Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 66:5 - Buku Lopatulika

5 Idzani, muone ntchito za Mulungu; zochitira Iye ana a anthu nzoopsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Idzani, muone ntchito za Mulungu; zochitira Iye ana a anthu nzoopsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Bwerani mudzaone zimene Mulungu wachita, ntchito zake nzodabwitsa pakati pa anthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Bwerani mudzaone zimene Mulungu wachita, ntchito zanu ndi zoopsa ndithu pakati pa anthu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 66:5
11 Mawu Ofanana  

zodabwitsa m'dziko la Hamu, zoopsa ku Nyanja Yofiira.


Ntchito za Yehova nzazikulu, zofunika ndi onse akukondwera nazo.


Idzani, penyani ntchito za Yehova, amene achita zopululutsa padziko lapansi.


Aletsa nkhondo ku malekezero a dziko lapansi; athyola uta, nadula nthungo; atentha magaleta ndi moto.


Atigonjetsera anthu, naika amitundu pansi pa mapazi athu.


Idzani, imvani, inu nonse akuopa Mulungu, ndipo ndidzafotokozera zonse anazichitira moyo wanga.


Nenani kwa Mulungu, Ha, ntchito zanu nzoopsa nanga! Chifukwa cha mphamvu yanu yaikulu adani anu adzagonjera Inu.


Alemekeze dzina lanu lalikulu ndi loopsa. Ili ndilo loyera.


Ndi mikombero yake inali yokuzika ndi yoopsa; ndi izi zinai zinali ndi mikombero yao yodzala ndi maso pozungulira pao.


Pakuti palibe nyanga pakati pa Yakobo, kapena ula mwa Israele; pa nyengo yake adzanena kwa Yakobo ndi Israele, chimene Mulungu achita.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa