Masalimo 66:11 - Buku Lopatulika11 Munapita nafe kuukonde; munatisenza chothodwetsa pamsana pathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Munapita nafe kuukonde; munatisenza chothodwetsa pamsana pathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Inu mudatiloŵetsa mu ukonde wa adani, mudatisenzetsa katundu wolemera pamsana pathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Inu mwatilowetsa mʼndende ndi kutisenzetsa zolemera pa misana yathu. Onani mutuwo |