Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 64:1 - Buku Lopatulika

1 Imvani Mulungu, mau anga, m'kudandaula kwanga; sungani moyo wanga angandiopse mdani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Imvani Yehova, mau anga, m'kudandaula kwanga; sungani moyo wanga angandiopse mdani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Imvani mau anga, Inu Mulungu, pamene ndikukudandaulirani. Tetezani moyo wanga kwa mdani woopsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ndimvereni Mulungu pomwe ndikunena madandawulo anga; tetezani moyo wanga ku chiopsezo cha mdani.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 64:1
13 Mawu Ofanana  

Ndilanditseni, Yehova, kwa munthu woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa;


Yehova, ndaitana kwa Inu; ndifulumireni ine; munditcherere khutu, pamene ndiitana kwa Inu.


Imvani, Yehova, liu langa pofuula ine; mundichitirenso chifundo ndipo mundivomereze.


Ndinafuna Yehova ndipo anandivomera, nandilanditsa m'mantha anga onse.


nanena, Usaope Paulo; ukaimirira pamaso pa Kaisara; ndipo, taona, Mulungu anakupatsa onse amene akuyenda nawe pamodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa