Masalimo 61:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti munakhala pothawirapo panga; nsanja yolimba pothawa mdani ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti munakhala pothawirapo panga; nsanja yolimba pothawa mdani ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Inutu ndinu kothaŵira kwanga, nsanja yolimba yonditeteza kwa adani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pakuti Inu mwakhala pothawirapo panga, nsanja yolimba polimbana ndi adani anga. Onani mutuwo |