Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 59:8 - Buku Lopatulika

8 Koma Inu, Yehova, mudzawaseka; mudzalalatira amitundu onse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Koma Inu, Yehova, mudzawaseka; mudzalalatira amitundu onse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Koma Inu Chauta, mumangoŵaseka. Inu mumanyozera anthu onse akunja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Koma Inu Yehova, mumawaseka, mumayinyoza mitundu yonseyo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 59:8
8 Mawu Ofanana  

Anena m'mtima mwake, Mulungu waiwala; wabisa nkhope yake; sapenya nthawi zonse.


Wokhala m'mwambayo adzaseka; Ambuye adzawanyoza.


Ambuye adzamseka, popeza apenya kuti tsiku lake likudza.


Mukwezeke m'mwambamwamba, Mulungu; ulemerero wanu ukhale pamwamba padziko lonse lapansi.


Ndinu Yehova, Mulungu wa makamu, Mulungu wa Israele. Ukani kukazonda amitundu onse, musachitire chifundo mmodzi yense wakuchita zopanda pake monyenga.


Inetu ndidzachitira chiphwete tsoka lanu, ndidzatonyola pakudza mantha anu;


Ndipo ngati iye samvera iwo, uuze Mpingo; ndipo ngati iye samveranso Mpingowo, akhale kwa iwe monga wakunja ndi wamsonkho.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa