Masalimo 59:7 - Buku Lopatulika7 Onani abwetuka pakamwa pao; m'milomo mwao muli lupanga, pakuti amati, Amva ndani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Onani abwetuka pakamwa pao; m'milomo mwao muli lupanga, pakuti amati, Amva ndani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Awo ali ukowo, akulongolola kwambiri, ndipo akufuula mwankhalwe, chifukwa m'maganizo mwao amati, “Ndani akutimva nanga?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Onani zomwe amalavula mʼkamwa mwawo; iwo amalavula malupanga kuchokera pa milomo yawo, ndipo amanena kuti, “Ndani angatimve?” Onani mutuwo |