Masalimo 59:6 - Buku Lopatulika6 Abwera madzulo, auwa ngati galu, nazungulira mzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Abwera madzulo, auwa ngati galu, nazungulira mudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Amabweranso madzulo aliwonse akuuwa ngati agalu, nkumangoyendayenda mu mzinda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwo amabweranso madzulo akuchita phokoso ngati agalu ndi kumangoyendayenda mu mzinda. Onani mutuwo |