Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 59:2 - Buku Lopatulika

2 Mundilanditse kwa ochita zopanda pake, ndipo ndipulumutseni kwa anthu olira mwazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mundilanditse kwa ochita zopanda pake, ndipo ndipulumutseni kwa anthu olira mwazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Pulumutseni kwa anthu ochita zoipa, landitseni kwa anthu okhetsa magazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Landitseni kwa anthu ochita zoyipa ndipo mundipulumutse kwa anthu okhetsa magazi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 59:2
6 Mawu Ofanana  

Indedi, mudzaomba woipa, Mulungu: Ndipo amuna inu okhumba mwazi, chokani kwa ine.


Musandichotsere mzimu wanga pamodzi ndi olakwa, kapena moyo wanga pamodzi ndi anthu okhetsa mwazi;


Pondifika ine ochita zoipa kudzadya mnofu wanga, inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa.


Koma Inu, Mulungu, mudzawatsitsira kudzenje la chionongeko. Anthu okhetsa mwazi ndi achinyengo masiku ao sadzafikira nusu; koma ine ndidzakhulupirira Inu.


kuti angamwetule moyo wanga ngati mkango, ndi kuukadzula, wopanda wina wondilanditsa.


Adzandiukira ndani kutsutsana nao ochita zoipa? Adzandilimbikira ndani kutsutsana nao ochita zopanda pake?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa