Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 55:8 - Buku Lopatulika

8 Ndikadafulumira ndipulumuke kumphepo yolimba ndi namondwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndikadafulumira ndipulumuke kumphepo yolimba ndi namondwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 “Ndikadafulumira kupeza pobisalira mphepo yaukali yamkunthoyi.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ndikanathamangira kumalo anga a chitetezo; kutali ndi mphepo yaukali ndi yamkuntho.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 55:8
4 Mawu Ofanana  

Zingwe za imfa zinandizinga, ndipo mitsinje ya zopanda pake inandiopsa.


Ndipo padzakhala chihema cha mthunzi, nthawi ya usana yopewera kutentha, pothawira ndi pousa mvula ndi mphepo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa