Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 55:7 - Buku Lopatulika

7 Onani, ndikadathawira kutali, ndikadagona m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Onani, ndikadathawira kutali, ndikadagona m'chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Inde, ndikadathaŵira kutali ndi kukakhala ku chipululu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndikanathawira kutali ndi kukakhala mʼchipululu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 55:7
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide ananena nao anyamata ake onse akukhala naye ku Yerusalemu, Nyamukani tithawe, tikapanda kuthawa palibe mmodzi wa ife adzapulumuka Abisalomu; fulumirani kuchoka, angatipeze msanga ndi kutigwetsera zoipa ndi kukantha mzinda ndi lupanga lakuthwa.


pamenepo Yeremiya anatuluka mu Yerusalemu kumuka kudziko la Benjamini, kukalandira gawo lake kumeneko.


Ha, mutu wanga ukadakhala madzi, ndi maso anga kasupe wa misozi, kuti usana ndi usiku ndilirire ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga!


Ha, ndikadakhala ndi chigono cha anthu aulendo m'chipululu; kuti ndisiye anthu anga, ndiwachokere, pakuti onse ali achigololo, msonkhano wa anthu achiwembu.


Ndipo Davide ananena mumtima mwake, Tsiku lina Saulo adzandipha; palibe china chondikomera koma kuti ndithawire ku dziko la Afilisti; ndipo Saulo adzakhala kakasi chifukwa cha ine, osandifunanso m'malire onse a Israele, momwemo ndidzapulumuka m'dzanja lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa