Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 55:6 - Buku Lopatulika

6 Ndipo ndinati, Ha, wina akadandipatsa mapiko onga a njiwa! Mwenzi nditauluka, ndi kukhaliratu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Ndipo ndinati, Ha, wina akadandipatsa mapiko onga a njiwa! Mwenzi nditauluka, ndi kukhaliratu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndipo ndimati, “Ndikadakhala ndi mapiko onga a njiŵa, bwenzi nditauluka kupita kutali kukapuma.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Ndinati, “Ndithu, ndikanakhala ndi mapiko ankhunda! Ndikanawulukira kutali ndi kukapuma.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 55:6
4 Mawu Ofanana  

Ndakhulupirira Yehova, mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame?


Ndikadzitengera mapiko a mbandakucha, ndi kukhala ku malekezero a nyanja;


Mtima wanga uguguda, mantha andiopsetsa ine; chizirezire chimene ndinachikhumba chandisandukira kunthunthumira.


Ndipo anapatsa mkazi mapiko awiri a chiombankhanga chachikulu, kuti akaulukire kuchipululu, ku mbuto yake, kumene adyetsedwako nthawi, ndi zinthawi, ndi nusu la nthawi, osapenya nkhope ya njoka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa