Masalimo 55:9 - Buku Lopatulika9 Aonongeni, Ambuye, gawani lilime lao, pakuti ndaona chiwawa ndi ndeu m'mzindamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Aonongeni, Ambuye, gawani lilime lao, pakuti ndaona chiwawa ndi ndeu m'mudzimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Inu Ambuye, onongani zolinga za adani anga, musokoneze upo wao. Pakuti ndikuwona anthu akuchita chiwawa ndi nkhondo mumzindamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Sokonezani maganizo a oyipa, Inu Ambuye, tsutsani mawu awo; pakuti ine ndikuona chiwawa ndi mkangano mu mzinda. Onani mutuwo |