Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 55:4 - Buku Lopatulika

4 Mtima wanga uwawa m'kati mwanga; ndipo zoopsa za imfa zandigwera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Mtima wanga uwawa m'kati mwanga; ndipo zoopsa za imfa zandigwera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Mtima wanga ukumva ululu woopsa, zoopsa za imfa zandigwera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mtima wanga ukupweteka mʼkati mwanga; mantha a imfa andigwera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 55:4
14 Mawu Ofanana  

Ndipo anatero Simei pakutukwana, Choka, choka, munthu wa mwazi iwe, woipa iwe;


Zingwe za imfa zinandizinga, ndi zowawa za manda zinandigwira: ndinapeza nsautso ndi chisoni.


Adani anga andinyoza ndi kundithyola mafupa anga; pakunena ndine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?


Moyo wanganso wanthunthumira kwakukulu; ndipo Inu, Yehova, kufikira liti?


Chotonza chandiswera mtima, ndipo ndidwala ine; ndipo ndinayembekeza wina wondichitira chifundo, koma palibe; ndinayembekeza onditonthoza mtima, osawapeza.


Pakuti mzimu wanga wadzala nao mavuto, ndi moyo wanga wayandikira kumanda.


Moyo wanga wavutika tsopano; ndipo ndidzanena chiyani? Atate, ndipulumutseni Ine kunthawi iyi. Koma chifukwa cha ichi ndinadzera nthawi iyi.


Ameneyo, m'masiku a thupi lake anapereka mapemphero ndi mapembedzero pamodzi ndi kulira kwakukulu ndi misozi kwa Iye amene anakhoza kumpulumutsa Iye muimfa, ndipo anamveka popeza anaopa Mulungu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa