Masalimo 55:3 - Buku Lopatulika3 chifukwa cha mau a mdani, chifukwa cha kundipsinja woipa; pakuti andisenza zopanda pake, ndipo adana nane mumkwiyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 chifukwa cha mau a mdani, chifukwa cha kundipsinja woipa; pakuti andisenza zopanda pake, ndipo adana nane mumkwiyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndikuda nkhaŵa chifukwa adani anga akundifuulira, anthu oipa akundipsinja. Akundivutitsa kwambiri, akundikwiyira kosalekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 chifukwa cha mawu a adani anga, chifukwa cha kupondereza kwa anthu oyipa; pakuti andidzetsera masautso ndipo akundizunza mu mkwiyo wawo. Onani mutuwo |