Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 55:2 - Buku Lopatulika

2 Mverani, ndipo mundiyankhe, ndiliralira m'kudandaula kwanga ndi kubuula;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Mverani, ndipo mundiyankhe, ndiliralira m'kudandaula kwanga ndi kubuula;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mundimvere, ndipo mundiyankhe. Mtima wanga suli m'malo chifukwa cha mavuto anga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 mverani ndipo mundiyankhe. Maganizo anga akundisautsa ndipo ndathedwa nzeru

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 55:2
12 Mawu Ofanana  

Yehova, imvani chilungamo, mverani mfuu wanga; tcherani khutu ku pemphero langa losatuluka m'milomo ya chinyengo.


Pamene ndinakhala chete mafupa anga anakalamba ndi kubuula kwanga tsiku lonse.


Ndapindika, ndawerama kwakukulu; ndimayenda woliralira tsiku lonse.


Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji? Ndimayenderanji woliralira chifukwa cha kundipsinja mdani?


Imvani Mulungu, mau anga, m'kudandaula kwanga; sungani moyo wanga angandiopse mdani.


Koma Mulungu anamvadi; anamvera mau a pemphero langa.


Ndikumbukira Mulungu ndipo ndivutika; ndilingalira ndipo mzimu wanga ukomoka.


Ndinalankhulalankhula ngati namzeze, pena chumba; Ndinalira maliro ngati nkhunda; maso anga analephera pogadamira kumwamba. Ambuye ndasautsidwa, mundiperekere chikoli.


Tonse tibangula ngati zilombo, ndi kulira maliro zolimba ngati nkhunda; tiyang'anira chiweruziro koma palibe; tiyang'anira chipulumutso koma chili patali ndi ife.


munamva mau anga; musabise khutu lanu popuma ndi pofuula ine.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa