Masalimo 55:1 - Buku Lopatulika1 Tcherani khutu pemphero langa, Mulungu; ndipo musadzibisa pa kupemba kwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Tcherani khutu pemphero langa, Mulungu; ndipo musadzibisa pa kupemba kwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Mulungu, tcherani khutu kuti mumve pemphero langa, musabisale pamene ndikukupembani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mvetserani pemphero langa, Inu Mulungu, musakufulatire kupempha kwanga, Onani mutuwo |