Masalimo 51:9 - Buku Lopatulika9 Muzibisire nkhope yanu zolakwa zanga, ndipo mufafanize mphulupulu zanga zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Muzibisire nkhope yanu zolakwa zanga, ndipo mufafanize mphulupulu zanga zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Mufulatire machimo anga, mufafanize zoipa zanga zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mufulatire machimo anga ndi kufafaniza zolakwa zanga zonse. Onani mutuwo |