Masalimo 51:10 - Buku Lopatulika10 Mundilengere mtima woyera, Mulungu; mukonze mzimu wokhazikika m'kati mwanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mundilengere mtima woyera, Mulungu; mukonze mzimu wokhazikika m'kati mwanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mundilengere mtima woyera, Inu Mulungu, muike mwa ine mtima watsopano ndi wokhazikika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mulenge mʼkati mwanga mtima woyera Inu Mulungu ndi kukonzanso mzimu wokhazikika mwa ine. Onani mutuwo |