Masalimo 50:9 - Buku Lopatulika9 Sindidzatenga ng'ombe m'nyumba mwako, kapena mbuzi m'makola mwako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Sindidzatenga ng'ombe m'nyumba mwako, kapena mbuzi m'makola mwako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndithudi, sindilandira ng'ombe kapena mbuzi iliyonse ya m'makola anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ine sindikufuna ngʼombe yayimuna kuchokera mʼkhola lako kapena mbuzi za mʼkhola lako, Onani mutuwo |