Masalimo 50:8 - Buku Lopatulika8 Sindikudzudzula iwe chifukwa cha nsembe zako; popeza nsembe zako zopsereza zili pamaso panga chikhalire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Sindikudzudzula iwe chifukwa cha nsembe zako; popeza nsembe zako zopsereza zili pamaso panga chikhalire. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Sindikudzudzulani chifukwa cha nsembe zanu, popeza kuti mumapereka nsembe zanu zopsereza kwa Ine nthaŵi zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Sindikudzudzula chifukwa cha nsembe zako, kapena nsembe zako zopsereza zimene zili pamaso panga nthawi zonse. Onani mutuwo |