Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 50:5 - Buku Lopatulika

5 Mundisonkhanitsire okondedwa anga, amene anapangana ndi Ine ndi nsembe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Mundisonkhanitsire okondedwa anga; amene anapangana ndi Ine ndi nsembe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Iye akuti, “Sonkhanitsani pamaso panga, anthu anga okhulupirika, amene adachita chipangano ndi Ine popereka nsembe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Mundisonkhanitsire okhulupirika anga, amene anachita pangano ndi ine pochita nsembe.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 50:5
17 Mawu Ofanana  

Imbirani Yehova, inu okondedwa ake, ndipo yamikani pokumbukira chiyero chake.


Inu okonda Yehova, danani nacho choipa: Iye asunga moyo wa okondedwa ake; awalanditsa m'manja mwa oipa.


kuti atchinjirize njira za chiweruzo, nadikire khwalala la opatulidwa ake.


Ine ndalamulira opatulidwa anga, inde, ndaitana amphamvu anga, achite mkwiyo wanga, okondwerera ndi ukulu wanga.


Pamenepo mudzathawa kudzera chigwa cha mapiri anga; pakuti chigwa cha mapiri chidzafikira ku Azali; ndipo mudzathawa monga umo munathawira chivomezi, masiku a Uziya mfumu ya Yuda; ndipo Yehova Mulungu wanga adzadza, ndi opatulika onse pamodzi ndi Inu.


Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwakukulu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa osankhidwa ake kumphepo zinai, kuyambira malekezero a thambo kufikira malekezero ake ena.


pakuti ichi ndi mwazi wanga wa pangano wothiridwa chifukwa cha anthu ambiri ku kuchotsa machimo.


kuti akakhazikitse mitima yanu yopanda chifukwa m'chiyero pamaso pa Mulungu Atate wathu, pakufika Ambuye wathu Yesu pamodzi ndi oyera mtima ake onse.


Ndipo tikupemphani, abale, chifukwa cha kudza kwake kwa Ambuye wathu Yesu Khristu, ndi kusonkhana pamodzi kwathu kwa Iye;


ndi kwa Yesu Nkhoswe ya chipangano chatsopano, ndi kwa mwazi wa kuwaza wakulankhula chokoma choposa mwazi wa Abele.


Koma Mulungu wa mtendere amene anabwera naye wotuluka mwa akufa Mbusa wamkulu wa nkhosa ndi mwazi wa chipangano chosatha, ndiye Ambuye wathu Yesu,


Ndipo kwa iwo, Enoki, wachisanu ndi chiwiri kuyambira kwa Adamu, ananenera kuti, Taona, wadza Ambuye ndi oyera ake zikwi makumi,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa