Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 49:12 - Buku Lopatulika

12 Koma munthu wa ulemu wake sakhalitsa, afanana ndi nyama zakuthengo, afanana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Koma munthu wa ulemu wake sakhalitsa, afanana ndi nyama za kuthengo, afanana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ngakhale munthu akhale wolemera chotani, komabe adzafa chabe ngati nyama zakuthengo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Ngakhale munthu akhale wachuma chotani, adzafa ngati nyama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 49:12
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Kaini anamdziwa mkazi wake; ndipo anatenga pakati, nabala Enoki: ndipo anamanga mzinda, nautcha dzina lake la mzindawo monga dzina la mwana wake, Enoki.


Onani, munaika masiku anga akhale monga kuyesa dzanja; ndipo zaka zanga zili ngati chabe pamaso panu, Indedi munthu aliyense angakhale wokhazikika, ali chabe konse.


Munthu waulemu, koma wosadziwitsa, afanana ndi nyama zakuthengo, afanana nazo.


Komatu mudzafa monga anthu, ndipo mudzagwa monga wina wa akulu.


Pakuti munthu sadziwatu mphindi yake; monga nsomba zigwidwa mu ukonde woipa, ndi mbalame zikodwa mumsampha, momwemo ana a anthu amagwidwa ndi nthawi ya tsoka, ngati msampha umene uwagwera modzidzimuka.


Popeza, Anthu onse akunga udzu, ndi ulemerero wao wonse ngati duwa la udzu. Udzuwo ungofota, ndi duwa lake lingogwa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa