Masalimo 45:6 - Buku Lopatulika6 Mpando wachifumu wanu, Mulungu, ukhala nthawi zonse zomka muyaya. Ndodo yachifumu ya ufumu wanu ndiyo ndodo yolunjika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mpando wachifumu wanu, Mulungu, ukhala nthawi zonse zomka muyaya. Ndodo yachifumu ya ufumu wanu ndiyo ndodo yolunjika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mpando wanu waufumu, Inu Mulungu, ndi wamuyaya, mumaweruza molungama mu ufumu wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mpando wanu waufumu, Inu Mulungu, udzakhala ku nthawi za nthawi; ndodo yaufumu yachilungamo idzakhala ndodo yaufumu ya ufumu wanu. Onani mutuwo |