Masalimo 45:3 - Buku Lopatulika3 Dzimangireni lupanga lanu m'chuuno mwanu, wamphamvu inu, ndi ulemerero wanu ndi ukulu wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Dzimangireni lupanga lanu m'chuuno mwanu, wamphamvu inu, ndi ulemerero wanu ndi ukulu wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Inu ngwazi yolimba mtima, mangirirani lupanga lanu m'chiwuno, mu ulemerero ndi ukulu wanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mangirirani lupanga lanu mʼchiwuno mwanu, inu munthu wamphamvu; mudziveke nokha ndi ulemerero ndi ukulu wanu. Onani mutuwo |