Masalimo 45:11 - Buku Lopatulika11 potero mfumuyo adzakhumba kukoma kwako, pakuti ndiye mbuye wako; ndipo iwe umgwadire iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 potero mfumuyo adzakhumba kukoma kwako, pakuti ndiye mbuye wako; ndipo iwe umgwadire iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mfumu idzakukonda chifukwa cha kukongola kwako. Umuŵeramire popeza kuti ndiye mbuyako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mfumu yathedwa nzeru chifukwa cha kukongola kwako; mulemekeze pakuti iyeyo ndiye mbuye wako. Onani mutuwo |