Masalimo 45:1 - Buku Lopatulika1 Mtima wanga usefukira nacho chinthu chokoma. Ndinena zopeka ine za mfumu, lilime langa ndilo peni yofulumiza kulemba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mtima wanga usefukira nacho chinthu chokoma. Ndinena zopeka ine za mfumu, lilime langa ndilo peni yofulumiza kulemba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mtima wanga wadzaza ndi nkhani yokoma. Ndikuimbira mfumu nyimbo yangayi. Lilime langa lili ngati cholembera cha katswiri wodziŵa kulemba bwino. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mtima wanga watakasika ndi nkhani yokoma pamene ndikulakatula mawu anga kwa mfumu; lilime langa ndi cholembera cha wolemba waluso. Onani mutuwo |