Masalimo 44:26 - Buku Lopatulika26 Ukani, tithandizeni, tiomboleni mwa chifundo chanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ukani, tithandizeni, tiomboleni mwa chifundo chanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Dzukani, mubwere kudzatithandiza. Tiwomboleni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Imirirani ndi kutithandiza, tiwomboleni chifukwa cha chikondi chanu chosasinthika. Onani mutuwo |