Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 44:6 - Buku Lopatulika

6 Pakuti uta wanga, ndipo lupanga langa silingandipulumutse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Pakuti sinditama uta wanga, ndipo lupanga langa silingandipulumutse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Sindidalira uta wanga, ngakhale lupanga langa silingandipulumutse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Sindidalira uta wanga, lupanga langa silindibweretsera chigonjetso;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 44:6
5 Mawu Ofanana  

Ena atama magaleta, ndi ena akavalo; koma ife tidzatchula dzina la Yehova Mulungu wathu.


Ndipo kunakhala, pamene Mose anakweza dzanja lake Israele anapambana; koma pamene anatsitsa dzanja lake Amaleke anapambana.


Koma ndidzachitira chifundo nyumba ya Yuda, ndi kuwapulumutsa mwa Ine Yehova Mulungu wao, osawapulumutsa ndi uta, kapena lupanga, kapena nkhondo ndi akavalo, kapena apakavalo.


Ndi msonkhano wonse uno udzazindikira kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga, kapena ndi mkondo; pakuti Yehova ndiye mwini nkhondo, ndipo Iye adzakuperekani inu m'manja athu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa