Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 42:7 - Buku Lopatulika

7 Madzi akuya aitanizana ndi madzi akuya, pa mkokomo wa matiti anu; mafunde onse a nyondonyondo anandimiza ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Madzi akuya aitanizana ndi madzi akuya, pa mkokomo wa matiti anu; mafunde onse a nyondonyondo anandimiza ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Madzi akuya akuitanizana ndi madzi akuyanso, mathithi anu akulindima kochititsa mantha. Mafunde anu ang'onoang'ono ndi akuluakulu omwe andimiza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Madzi akuya akuyitana madzi akuya mu mkokomo wa mathithi anu; mafunde anu onse obwera mwamphamvu andimiza.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 42:7
10 Mawu Ofanana  

Mundikonzeranso mboni zonditsutsa, ndi kundichulukitsira mkwiyo wanu; nkhondo yobwerezabwereza yandigwera.


Mkwiyo wanu utsamira pa ine, ndipo munandizunza ine ndi mafunde anu onse.


Alalikira chipasuko chilalikire; pakuti dziko lonse lafunkhidwa; mahema anga afunkhidwa dzidzidzi, ndi nsalu zanga zotchinga m'kamphindi.


Lidzafika tsoka lotsatanatsatana, kudzakhalanso mbiri yotsatanatsatana, ndipo adzafunafuna masomphenya a mneneri, koma malamulo adzatayikira wansembe, uphungu ndi kutayikira akulu.


Pakuti munandiponya mwakuya m'kati mwa nyanja, ndipo madzi anandizinga; mafunde anu onse a nyondonyondo anandimiza.


Ndipo muja tinalanda dziko m'manja mwa mafumu awiri a Aamori okhala tsidya lija la Yordani, kuyambira mtsinje wa Arinoni kufikira phiri la Heremoni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa