Masalimo 42:3 - Buku Lopatulika3 Misozi yanga yakhala ngati chakudya changa, usana ndi usiku; pakunena iwo kwa ine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Misozi yanga yakhala ngati chakudya changa, usana ndi usiku; pakunena iwo kwa ine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ntchito yanga ndi kulira usana ndi usiku, osalaŵa chakudya chilichonse. Ndipo anthu akhala akunena kuti, “Mulungu wako ali kuti?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Misozi yanga yakhala chakudya changa usana ndi usiku, pamene anthu akunena kwa ine tsiku lonse kuti, “Mulungu wako ali kuti?” Onani mutuwo |