Masalimo 42:1 - Buku Lopatulika1 Monga nswala ipuma wefuwefu kukhumba mitsinje; motero moyo wanga upuma wefuwefu kukhumba Inu, Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Monga nswala ipuma wefuwefu kukhumba mitsinje; motero moyo wanga upuma wefuwefu kukhumba Inu, Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Monga momwe mbaŵala imakhumbira mtsinje wamadzi, ndimo m'mene mtima wanga umakhumbira Inu Mulungu wanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Monga mbawala ipuma wefuwefu kufunafuna mitsinje yamadzi, kotero moyo wanga upuma wefuwefu kufunafuna Inu Mulungu. Onani mutuwo |