Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 41:11 - Buku Lopatulika

11 Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine, popeza mdani wanga sandiseka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Umo ndidziwa kuti mukondwera ndi ine, popeza mdani wanga sandiseka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Mukatero ndidzadziŵa kuti mumakondwera nane, chifukwa mdani wanga sadandipambane.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ine ndikudziwa kuti mukukondwera nane, pakuti mdani wanga sandigonjetsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 41:11
9 Mawu Ofanana  

Alemekezedwe Yehova, amene sanatipereke kumano kwao tikhale chakudya chao.


kuti anganene mdani wanga, Ndamgonjetsa; ndipo angakondwere otsutsana nane posunthika ine.


Yehova akondwera nao akumuopa Iye, iwo akuyembekeza chifundo chake.


Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu, ndisachite manyazi; adani anga asandiseke ine.


Ndipo simunandipereke m'dzanja la mdani; munapondetsa mapazi anga pali malo.


Asanene mumtima mwao, Hede, momwemo! Asanene, Tammeza iye.


Mundichitire chizindikiro choti chabwino; kuti ondida achione, nachite manyazi, popeza Inu, Yehova, munandithandiza ndi kundisangalatsa.


Muimbire Yehova, mulemekeze Yehova; pakuti walanditsa moyo wa aumphawi m'dzanja la ochita zoipa.


atavula maukulu ndi maulamuliro, anawaonetsera poyera, nawagonjetsera nako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa