Masalimo 41:10 - Buku Lopatulika10 Koma Inu, Yehova, mundichitire chifundo, ndipo mundiutse, kuti ndiwabwezere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma Inu, Yehova, mundichitire chifundo, ndipo mundiutse, kuti ndiwabwezere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Koma Inu Chauta, mundikomere mtima, mundichiritse kuti ndiŵalange anthuwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Koma Yehova mundichititre chifundo, dzutseni kuti ndiwabwezere. Onani mutuwo |