Masalimo 40:7 - Buku Lopatulika7 Pamenepo ndinati, Taonani, ndadza; m'buku mwalembedwa za Ine, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Pamenepo ndinati, Taonani, ndadza; m'buku mwalembedwa za Ine, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tsono ndidati, “Ndilipo, ndikubwera, monga zidalembedwa za ine m'buku la malamulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kotero ndinati, “Ndili pano, ndabwera. Mʼbuku mwalembedwa za ine. Onani mutuwo |