Masalimo 39:4 - Buku Lopatulika4 Yehova, mundidziwitse chimaliziro changa, ndi mawerengedwe a masiku anga ndi angati; ndidziwe malekezero anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Yehova, mundidziwitse chimaliziro changa, ndi mawerengedwe a masiku anga ndi angati; ndidziwe malekezero anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 “Inu Chauta, mundidziŵitse mathero a moyo wanga, mundidziŵitse kuchepa kwa masiku anga. Mundilangize kuti moyo wanga sukhalira kutha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Yehova ndionetseni mathero a moyo wanga ndi chiwerengero cha masiku anga; mundidziwitse kuti moyo wanga ndi wosakhalitsa motani. Onani mutuwo |