Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 39:3 - Buku Lopatulika

3 Mtima wanga unatentha m'kati mwa ine; unayaka moto pakulingirira ine. Pamenepo ndinalankhula ndi lilime langa,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mtima wanga unatentha m'kati mwa ine; unayaka moto pakulingirira ine. Pamenepo ndinalankhula ndi lilime langa,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mtima wanga udavutika, ndipo pamene ndidasinkhasinkha, mtima wanga udangoyaka moto. Pompo ndidalankhula ndi mau akuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Mtima wanga unatentha mʼkati mwanga, ndipo pamene ndinkalingalira, moto unayaka; kenaka ndinayankhula ndi lilime langa:

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 39:3
3 Mawu Ofanana  

Ndipo ngati nditi, Sindidzamtchula Iye, sindidzanenanso m'dzina lake, pamenepo m'mtima mwanga muli ngati moto wotentha wotsekedwa m'mafupa anga, ndipo ndalema ndi kupirira, sindingathe kupiriranso.


M'mwemo mzimu unandinyamula ndi kuchoka nane; ndipo ndinamuka wowawidwa, womyuka mtima; koma dzanja la Yehova linandigwirizitsa.


Ndipo anati wina kwa mnzake, Mtima wathu sunali wotentha m'kati mwathu nanga m'mene analankhula nafe m'njira, m'mene anatitsegulira malembo?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa